This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. “Hawu! Hawu! Hawu! Weza Nayo!” Iyo idali mfuu ya angoni omwe Loweruka adasonkhana m’boma la Dedza kukachitira umboni kudzozedwa kwa Zonyera Zambuzi. A Enoch Zonyera Zambuzi Kalapino, adzozedwa mwachikhalidwe cha Angoni kukhala iNkosi Kachindamoto VIII m’boma la Dedza. A Zonyera omwe ali ndi zaka 61, awadzodza kutsatira imfa ya a Tereza Kachindamoto ndipo mwambowu unachitikira […] Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Business and Finance
Wadzozedwa Zonyera Zambuzi